Yeremiya 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Cholowa changacho chasanduka chipululu, Ndipo chafota.*Chawonongeka pamaso panga,+ Dziko lonse lakhala bwinja,Koma palibe aliyense amene zikumukhudza.+
11 Cholowa changacho chasanduka chipululu, Ndipo chafota.*Chawonongeka pamaso panga,+ Dziko lonse lakhala bwinja,Koma palibe aliyense amene zikumukhudza.+