-
Yeremiya 13:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ukawauzenso uthenga wakuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo.”’ Ukakawauza zimenezi akakufunsa kuti, ‘Kodi ife sitikudziwa kuti mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo?’
-