Yeremiya 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano uwauze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo.”’+ Ukakawauza zimenezi, iwo adzakufunsa kuti, ‘Kodi ife sitikudziwa kuti mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo?’ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:12 Galamukani!,9/2015, tsa. 7
12 “Tsopano uwauze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo.”’+ Ukakawauza zimenezi, iwo adzakufunsa kuti, ‘Kodi ife sitikudziwa kuti mtsuko uliwonse waukulu amadzazamo vinyo?’