Yeremiya 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kodi Mkusi* angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa,Mungathe kuchita zinthu zabwino.
23 “Kodi Mkusi* angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa,Mungathe kuchita zinthu zabwino.