Yeremiya 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kodi Mkusi*+ angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa mungathe kuchita zinthu zabwino.+
23 “Kodi Mkusi*+ angasinthe khungu lake, kapena kodi kambuku angasinthe mawanga ake?+ Ngati angathe kuchita zimenezi, ndiye kuti inunso amene munaphunzitsidwa kuchita zinthu zoipa mungathe kuchita zinthu zabwino.+