-
Yeremiya 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma chiwiya chimene woumba mbiyayo ankapanga ndi dongo chinawonongeka mʼmanja mwake. Choncho iye anasintha nʼkupanga chiwiya china ndi dongo lomwelo, malinga ndi zimene anaona kuti nʼzabwino.
-