Yeremiya 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chiwiya chimene anali kupanga ndi dongo chinawonongeka ndi dzanja la woumbayo. Choncho iye anasintha ndipo anapanga chiwiya china ndi dongo lomwelo malinga ndi zimene anaona kuti n’zabwino.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:4 Nsanja ya Olonda,4/1/1999, tsa. 22
4 Chiwiya chimene anali kupanga ndi dongo chinawonongeka ndi dzanja la woumbayo. Choncho iye anasintha ndipo anapanga chiwiya china ndi dongo lomwelo malinga ndi zimene anaona kuti n’zabwino.+