Yeremiya 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi sinowo wamʼmapiri a ku Lebanoni amasungunuka* nʼkuchoka pamiyala yake? Kapena kodi madzi ozizira bwino amene akuyenda kuchokera kutali adzauma?
14 Kodi sinowo wamʼmapiri a ku Lebanoni amasungunuka* nʼkuchoka pamiyala yake? Kapena kodi madzi ozizira bwino amene akuyenda kuchokera kutali adzauma?