-
Yeremiya 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kodi chipale chofewa chidzasungunuka ndi kuchoka pamapiri a ku Lebanoni? Kapena kodi madzi ochokera kudziko lina ozizira bwino, amene akudontha, adzauma?
-