Yeremiya 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo anagwira Uliya nʼkubwera naye kwa Mfumu Yehoyakimu. Ndiyeno mfumuyo inapha Uliya ndi lupanga+ nʼkutaya mtembo wake mʼmanda a anthu wamba.”
23 Iwo anagwira Uliya nʼkubwera naye kwa Mfumu Yehoyakimu. Ndiyeno mfumuyo inapha Uliya ndi lupanga+ nʼkutaya mtembo wake mʼmanda a anthu wamba.”