Yeremiya 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kumeneko anthuwo anagwira Uliya ndi kubwera naye kwa Mfumu Yehoyakimu. Ndiyeno mfumuyo inapha Uliya ndi lupanga+ ndi kutaya mtembo wake m’manda a anthu wamba.”
23 Kumeneko anthuwo anagwira Uliya ndi kubwera naye kwa Mfumu Yehoyakimu. Ndiyeno mfumuyo inapha Uliya ndi lupanga+ ndi kutaya mtembo wake m’manda a anthu wamba.”