26 ‘Yehova wakuika kuti ukhale wansembe mʼmalo mwa Yehoyada wansembe, kuti ukhale woyangʼanira mʼnyumba ya Yehova komanso kuti uzimanga munthu aliyense wamisala, amene akuchita zinthu ngati mneneri ndipo uzimuika mʼmatangadza, miyendo, manja ndi mutu womwe.+