Yeremiya 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Uli ndi tsogolo labwino,+ Ndipo ana ako adzabwerera kudziko lawo,’ akutero Yehova.”+