Yeremiya 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ndinkawayangʼanitsitsa kuti ndiwazule, ndiwagwetse, ndiwapasule, ndiwawononge komanso kuti ndiwasakaze.+ Mofanana ndi zimenezi, ndidzawayangʼanitsitsanso kuti ndiwamange komanso ndiwadzale,”+ akutero Yehova.
28 “Ndinkawayangʼanitsitsa kuti ndiwazule, ndiwagwetse, ndiwapasule, ndiwawononge komanso kuti ndiwasakaze.+ Mofanana ndi zimenezi, ndidzawayangʼanitsitsanso kuti ndiwamange komanso ndiwadzale,”+ akutero Yehova.