Yeremiya 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yehonadabu mwana wa Rekabu analamula ana ake kuti asamamwe vinyo ndipo iwo akhala akutsatira mawu ake moti samwa vinyo mpaka lero pomvera lamulo la kholo lawo.+ Koma ine ndakhala ndikulankhula nanu mobwerezabwereza,* koma simunandimvere.+
14 “Yehonadabu mwana wa Rekabu analamula ana ake kuti asamamwe vinyo ndipo iwo akhala akutsatira mawu ake moti samwa vinyo mpaka lero pomvera lamulo la kholo lawo.+ Koma ine ndakhala ndikulankhula nanu mobwerezabwereza,* koma simunandimvere.+