-
Yeremiya 35:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Anthu a m’nyumba ya Rekabu akhala akutsatira mawu a Yehonadabu mwana wa Rekabu,+ amene analamula ana ake kuti asamwe vinyo, ndipo sanamwe vinyo kufikira lerolino. Iwo achita zimenezi chifukwa chomvera lamulo la kholo lawo.+ Koma ine ndinali kulankhula nanu anthu inu, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kulankhula nanu,+ koma simunandimvere.+
-