-
Yeremiya 39:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 ‘Koma pa tsikulo iweyo ndidzakupulumutsa ndipo sudzaperekedwa mʼmanja mwa anthu amene ukuwaopa,’ akutero Yehova.
-