Yeremiya 39:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Pa tsikulo ndidzakulanditsa+ ndipo sudzaperekedwa m’manja mwa anthu amene umawaopa,’+ watero Yehova. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:17 Nsanja ya Olonda,5/1/2012, tsa. 31
17 “‘Pa tsikulo ndidzakulanditsa+ ndipo sudzaperekedwa m’manja mwa anthu amene umawaopa,’+ watero Yehova.