-
Yeremiya 40:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiye Ayuda onse amene anali ku Mowabu, ku Amoni, ku Edomu komanso amene anali mʼmayiko ena onse anamvanso kuti mfumu ya Babulo yalola kuti anthu amene anatsala azikhala ku Yuda komanso kuti yaika Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani kuti aziwalamulira.
-