Yeremiya 40:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Gedaliya+ mwana wa Ahikamu anauza Yohanani mwana wa Kareya kuti: “Usachite zimenezi chifukwa zimene ukunena zokhudza Isimaeli, ndi zabodza.”
16 Koma Gedaliya+ mwana wa Ahikamu anauza Yohanani mwana wa Kareya kuti: “Usachite zimenezi chifukwa zimene ukunena zokhudza Isimaeli, ndi zabodza.”