Yeremiya 40:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ anauza Yohanani mwana wa Kareya kuti: “Usachite zimenezi. Zimene ukunena zokhudza Isimaeli si zoona.”+
16 Koma Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ anauza Yohanani mwana wa Kareya kuti: “Usachite zimenezi. Zimene ukunena zokhudza Isimaeli si zoona.”+