-
Yeremiya 41:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ananyamuka ku Mizipa akulira kuti akakumane nawo. Atakumana nawo anawauza kuti: “Tiyeni kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu.”
-