Yeremiya 41:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ananyamuka ku Mizipa akulira kuti akakumane nawo.+ Atakumana nawo anawauza kuti: “Tiyeni kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu.”
6 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ananyamuka ku Mizipa akulira kuti akakumane nawo.+ Atakumana nawo anawauza kuti: “Tiyeni kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu.”