Yeremiya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anachita zimenezi chifukwa cha Akasidi. Iwo ankaopa Akasidiwo chifukwa chakuti Isimaeli mwana wa Netaniya anapha Gedaliya mwana wa Ahikamu, amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira mʼdzikolo.+
18 Anachita zimenezi chifukwa cha Akasidi. Iwo ankaopa Akasidiwo chifukwa chakuti Isimaeli mwana wa Netaniya anapha Gedaliya mwana wa Ahikamu, amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira mʼdzikolo.+