Yeremiya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anachita zimenezi chifukwa cha Akasidi.+ Iwo anali kuopa Akasidiwo+ chifukwa chakuti Isimaeli mwana wa Netaniya anapha Gedaliya mwana wa Ahikamu+ amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+
18 Anachita zimenezi chifukwa cha Akasidi.+ Iwo anali kuopa Akasidiwo+ chifukwa chakuti Isimaeli mwana wa Netaniya anapha Gedaliya mwana wa Ahikamu+ amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+