-
Yeremiya 42:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mneneri Yeremiya anawayankha kuti: “Ndamva zimene mwanenazo. Ndipemphera kwa Yehova Mulungu wanu malinga ndi zimene mwapempha. Ndipo mawu aliwonse amene Yehova angakuyankheni ndidzakuuzani. Sindidzakubisirani chilichonse.”
-