Yeremiya 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mneneri Yeremiya anawayankha kuti: “Ndamva zimene mwanenazo. Ndipemphera kwa Yehova Mulungu wanu malinga ndi zimene mwapempha.+ Ndipo mawu aliwonse amene Yehova angakuyankheni ndidzakuuzani.+ Sindidzakubisirani kalikonse.”+
4 Pamenepo mneneri Yeremiya anawayankha kuti: “Ndamva zimene mwanenazo. Ndipemphera kwa Yehova Mulungu wanu malinga ndi zimene mwapempha.+ Ndipo mawu aliwonse amene Yehova angakuyankheni ndidzakuuzani.+ Sindidzakubisirani kalikonse.”+