-
Yeremiya 42:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Iwo anayankha Yeremiya kuti: “Yehova akhale mboni yoona ndi yokhulupirika, ndipo atilange ngati sitidzachita ndendende mogwirizana ndi malangizo amene Yehova Mulungu wako angatipatse kudzera mwa iwe.
-