Yeremiya 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno iwo anauza Yeremiya kuti: “Yehova akhale mboni yoona ndi yokhulupirika, ndipo atilange+ ngati sitidzachita ndendende mogwirizana ndi mawu onse amene Yehova Mulungu wako angakutume kwa ife.+
5 Ndiyeno iwo anauza Yeremiya kuti: “Yehova akhale mboni yoona ndi yokhulupirika, ndipo atilange+ ngati sitidzachita ndendende mogwirizana ndi mawu onse amene Yehova Mulungu wako angakutume kwa ife.+