Yeremiya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yeremiya anaitana Yohanani mwana wa Kareya, pamodzi ndi akuluakulu onse a asilikali amene anali naye. Anaitananso anthu onse, anthu wamba ndi anthu olemekezeka omwe.+
8 Choncho Yeremiya anaitana Yohanani mwana wa Kareya, pamodzi ndi akuluakulu onse a asilikali amene anali naye. Anaitananso anthu onse, anthu wamba ndi anthu olemekezeka omwe.+