Yeremiya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Yeremiya anaitana Yohanani mwana wa Kareya, pamodzi ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali naye. Anaitananso anthu ena onse osasiyapo aliyense.+
8 Kenako Yeremiya anaitana Yohanani mwana wa Kareya, pamodzi ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali naye. Anaitananso anthu ena onse osasiyapo aliyense.+