Yeremiya 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Ndidzakuchitirani chifundo+ moti mfumuyo idzakumverani chifundo nʼkukubwezerani kudziko lanu.