Yeremiya 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzakuchitirani chifundo moti mfumuyo idzakumverani chifundo ndi kukubwezerani kudziko lanu.+