Yeremiya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo amuna onse amene atsimikiza mtima kupita ku Iguputo kuti akakhale kumeneko adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.* Palibe amene adzapulumuke kapena kuthawa tsoka limene ndidzawagwetsere.”’
17 Ndipo amuna onse amene atsimikiza mtima kupita ku Iguputo kuti akakhale kumeneko adzafa ndi lupanga, njala ndi mliri.* Palibe amene adzapulumuke kapena kuthawa tsoka limene ndidzawagwetsere.”’