Yeremiya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna onse amene atsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo monga alendo ndiwo adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+ Pakati pawo sipadzapezeka wopulumuka kapena wothawa chifukwa ndidzawagwetsera tsoka.”’+
17 Amuna onse amene atsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo monga alendo ndiwo adzafa ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+ Pakati pawo sipadzapezeka wopulumuka kapena wothawa chifukwa ndidzawagwetsera tsoka.”’+