Yeremiya 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti zolakwa zanu zidzakuphetsani. Zili choncho chifukwa inu munandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanene ndipo ife tidzachita zomwezo.’+
20 kuti zolakwa zanu zidzakuphetsani. Zili choncho chifukwa inu munandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanene ndipo ife tidzachita zomwezo.’+