Yeremiya 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti mwachimwira miyoyo yanu.+ Zili choncho chifukwa inu mwandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena ndipo ife tidzachita zomwezo.’+
20 kuti mwachimwira miyoyo yanu.+ Zili choncho chifukwa inu mwandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena ndipo ife tidzachita zomwezo.’+