-
Yeremiya 43:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Tenga miyala ikuluikulu ndipo ukaibise mʼdothi limene anamangira masitepe a njerwa amene ali pakhomo la nyumba ya Farao ku Tahapanesi. Ukachite zimenezi amuna onse a Chiyuda akuona.
-