Yeremiya 43:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tenga miyala ikuluikulu ndipo ukaibise m’dothi limene anamangira chiunda cha njerwa chimene chili pakhomo la nyumba ya Farao ku Tahapanesi. Ukachite zimenezi amuna onse achiyuda akuona.+
9 “Tenga miyala ikuluikulu ndipo ukaibise m’dothi limene anamangira chiunda cha njerwa chimene chili pakhomo la nyumba ya Farao ku Tahapanesi. Ukachite zimenezi amuna onse achiyuda akuona.+