Yeremiya 46:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko la Iguputo likubwera ngati mtsinje wa Nailo,+Likubwera ngati mitsinje ya madzi amphamvu,Ndipo likunena kuti, ‘Ndipita kukaphimba dziko lapansi. Ndikawononga mzinda ndi onse amene akukhala mumzindawo.’
8 Dziko la Iguputo likubwera ngati mtsinje wa Nailo,+Likubwera ngati mitsinje ya madzi amphamvu,Ndipo likunena kuti, ‘Ndipita kukaphimba dziko lapansi. Ndikawononga mzinda ndi onse amene akukhala mumzindawo.’