Yeremiya 46:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko la Iguputo likubwera ngati mtsinje wa Nailo,+ ndipo likubwera ngati madzi owinduka a m’mitsinje.+ Dzikolo likunena kuti, ‘Ndipita ndipo ndiphimba dziko lapansi. Ndiwononga mzinda ndi onse okhala mumzindawo.’+
8 Dziko la Iguputo likubwera ngati mtsinje wa Nailo,+ ndipo likubwera ngati madzi owinduka a m’mitsinje.+ Dzikolo likunena kuti, ‘Ndipita ndipo ndiphimba dziko lapansi. Ndiwononga mzinda ndi onse okhala mumzindawo.’+