-
Yeremiya 48:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 ‘Choncho masiku akubwera,’ akutero Yehova, ‘pamene ndidzawatumizire anthu kuti awapendeketse. Adzawapendeketsa nʼkuwakhuthula ngati vinyo mʼziwiya zawo ndipo adzaswa mitsuko yawo ikuluikulu kukhala mapalemapale.
-