Yeremiya 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Choncho masiku adzafika,’ watero Yehova, ‘ndipo ndidzawatumizira anthu opendeketsa mitsuko ndipo adzawapendeketsa.+ Iwo adzawatsanula m’ziwiya zawo ndipo adzaswa mitsuko yawo ikuluikulu kukhala mapalemapale.
12 “‘Choncho masiku adzafika,’ watero Yehova, ‘ndipo ndidzawatumizira anthu opendeketsa mitsuko ndipo adzawapendeketsa.+ Iwo adzawatsanula m’ziwiya zawo ndipo adzaswa mitsuko yawo ikuluikulu kukhala mapalemapale.