Yeremiya 48:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 ‘Nʼchifukwa chake mtima wanga udzalirire* Mowabu ngati chitoliro,*+Mtima wanga udzalirira* amuna a ku Kiri-haresi ngati chitoliro.* Chifukwa chuma chimene wapanga chidzawonongeka.
36 ‘Nʼchifukwa chake mtima wanga udzalirire* Mowabu ngati chitoliro,*+Mtima wanga udzalirira* amuna a ku Kiri-haresi ngati chitoliro.* Chifukwa chuma chimene wapanga chidzawonongeka.