Yeremiya 48:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 ‘Choncho mtima wanga udzachitira Mowabu phokoso ngati zitoliro.+ Mtima wanga udzachitira phokoso amuna a ku Kiri-haresi+ ngati zitoliro. Chotero zinthu zochuluka zimene wapanga zidzawonongeka.+
36 ‘Choncho mtima wanga udzachitira Mowabu phokoso ngati zitoliro.+ Mtima wanga udzachitira phokoso amuna a ku Kiri-haresi+ ngati zitoliro. Chotero zinthu zochuluka zimene wapanga zidzawonongeka.+