-
Yeremiya 48:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 ‘Taonani, Mowabu wachita mantha kwambiri. Lirani mofuula!
Mowabu wabwerera mwamanyazi.
Mowabu wasanduka chinthu choyenera kunyozedwa,
Komanso chochititsa mantha kwa anthu onse amene amuzungulira.’
-