Yeremiya 48:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ‘Mowabu wachita mantha. Lirani mofuula anthu inu! Mowabu watembenuka ndipo wachita manyazi.+ Mowabu wasanduka chinthu chonyozeka ndi chochititsa mantha kwa onse omuzungulira.’”
39 ‘Mowabu wachita mantha. Lirani mofuula anthu inu! Mowabu watembenuka ndipo wachita manyazi.+ Mowabu wasanduka chinthu chonyozeka ndi chochititsa mantha kwa onse omuzungulira.’”