-
Yeremiya 48:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 ‘Aliyense amene akuthawa chifukwa cha mantha adzagwera mʼdzenje,
Ndipo aliyense amene akutuluka mʼdzenjemo adzagwidwa mumsampha.
Chifukwa ndidzapereka chilango kwa anthu a ku Mowabu mʼchaka chimene ndasankha,’ akutero Yehova.
-