Yeremiya 48:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+ “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova.
44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+ “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova.