-
Yeremiya 49:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma ine ndidzawononga zinthu zonse za Esau nʼkumusiya alibe chilichonse.
Ndidzavundukula malo ake amene amabisalako,
Moti sadzathanso kubisala.
-